(DOWNLOAD) "Mpingo Waukulu" by Dag Heward-Mills * Book PDF Kindle ePub Free

eBook details
- Title: Mpingo Waukulu
- Author : Dag Heward-Mills
- Release Date : January 13, 2019
- Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
- Pages : * pages
- Size : 856 KB
Description
ââŠTuluka, nupite kumiseu ndi njira za kuminda, nuwaumirize anthu alowe. KUTI NYUMBA YANGA IDZALE.â Luka 14:23. Kulira kwa Mulungu ndi kwakuti dziko lonse lipulumutsidwe, ndi kuti nyumba Yake-tchalitchi-lidzale!
Kuchokera ku vumbulutso limeneri bukhu iri linabwera., âMpingo Waukuluâ lolembedwa ndi Bishop Dag Heward-Mills, mâbusa wa umodzi mwa mipingo yaikulu kwambiri ku Ghana. Mpingo wanu ndi utumiki wanu sudzakhalanso chimodzi modzi mukawerenga bukhu lolimbikitsali!âDr. Heward-Mills ndi wodzipereka kwa Ambuye Yesu Khristu ndi ntchito yotenga mbali pa kulalikira ku dziko lonse. Ndi mtsogoleri wamphamvu ndinso chitsanzo ku mautumiki onse, ndipo ife ku âChurch Growth Internationalâ, ndife olemekezedwa kudziwa ndikumutcha Dr. Dag Heward-Mills mnzathu komanso wogwira naye limodzi ntchito mu kholola lalikulu mu minda ya padziko.â
-Dr. Yonggi Cho
Wamkulu, Church Growth International